Deuteronomo 25:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali, kuti woyamba kubadwa amene adzambala, adzalowa dzina lace la mbale wace wafayo, kuti dzina lace lisafafanizidwe m'Israyeli.

Deuteronomo 25

Deuteronomo 25:1-12