Deuteronomo 24:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akampeza munthu waba mbale wace wina wa ana a Israyeli, namuyesa kapolo, kapena wamgulitsa, afe wakubayo; potero muzicotsa coipaco pakati panu.

Deuteronomo 24

Deuteronomo 24:1-13