Deuteronomo 24:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akatenga mkazi akhale wace, kudzali, ngati sapeza ufulu pamaso pace, popeza anapeza mwa iye kanthu kosayenera, amlembere kalata wa cilekanitso, ndi kumpereka uyu m'dzanja lace, ndi kumturutsa m'nyumba mwace.

Deuteronomo 24

Deuteronomo 24:1-4