Deuteronomo 22:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mkazi asabvale cobvala ca mwa muna, kapena mwamuna asabvale cobvala ca mkazi; pakuti ali yense wakucita izi Yehova Mulungu wanu anyansidwa naye.

Deuteronomo 22

Deuteronomo 22:1-6