Deuteronomo 22:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati mbale wanu sakhala pafupi ndi inu, kapena mukapanda kumdziwa, mubwere nayo kwanu ku nyumba yanu, kuti ikhale kwanu, kufikira mbale wanu akaifuna, ndipo wambwezera iyo.

Deuteronomo 22

Deuteronomo 22:1-5