Deuteronomo 21:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akakhala naye mwana wamwamuna wopulukira, ndi wopikisana naye, wosamvera mau a atate wace, kapena mau a mai wace, wosawamvera angakhale anamlanga;

Deuteronomo 21

Deuteronomo 21:12-23