Deuteronomo 2:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiwo anthu akuru, ndi ambiri, ndi atalitali, monga Aanaki; koma Yehova anawaononga pamaso pao; ndipo analanda dziko lao, nakhala m'malo mwao;

Deuteronomo 2

Deuteronomo 2:14-28