Deuteronomo 19:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mudzikonzere njira, ndi kugawa malire a dziko lanu, limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanu lanu, patatu; kuti wakupha munthu athawireko.

Deuteronomo 19

Deuteronomo 19:2-8