Deuteronomo 18:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mneneri wakucita modzikuza ndi kunena mau m'dzina langa, amene sindinamlamulira anene, kapena kunena m'dzina la milungu yina, mneneri ameneyo afe.

Deuteronomo 18

Deuteronomo 18:18-21