Deuteronomo 17:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akapeza pakati panu, m'mudzi wanu wina umene anakupatsani Yehova Mulungu wanu, wamwamuna kapena wamkazi wakucita ciri coipa pamaso pa Yehova Mulungu wanu, ndi kulakwira cipangano cace,

Deuteronomo 17

Deuteronomo 17:1-5