Deuteronomo 17:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mutakalowa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani, ndi kulilandira lanu lanu, ndi kukhalamo; ndipo mukanena, Tidziikire mfumu, monga amitundu onse akutizinga;

Deuteronomo 17

Deuteronomo 17:5-19