Deuteronomo 16:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cilungamo, cilungamo ndico muzicitsata, kuti mukhale ndi moyo ndi kulandira dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani.

Deuteronomo 16

Deuteronomo 16:19-22