Deuteronomo 15:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiko kuti pasakhale waumphawi mwa inu; pakuti Yehova adzakudalitsani kwambiri m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale colowa canu canu;

Deuteronomo 15

Deuteronomo 15:1-7