Deuteronomo 15:22-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Muidye m'mudzi mwanu; odetsa ndi oyera aidye cimodzimodzi, monga mphoyo ndi nswala.

23. Mwazi wace wokha musamadya; muuthire pansi ngati madzi.

Deuteronomo 15