Deuteronomo 14:13-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. ndi kamtema, ndi mphamba, ndi muimba monga mwa mtundu wace;

14. ndi khungubwe ali yense monga mwa mtundu wace;

15. ndi nthiwatiwa, ndi cipudo, ndi kakoa, ndi kabawi monga mwa mtundu wace;

16. ndi nkhutukutu, ndi mancici, ndi tsekwe;

Deuteronomo 14