Deuteronomo 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awa ndi malemba ndi maweruzo, muziwasamalirawa kuwacita m'dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu anakupatsani likhale lanu lanu, masiku onse akukhala ndi moyo inu pa dziko lapansi.

Deuteronomo 12

Deuteronomo 12:1-8