Deuteronomo 11:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma temberero, ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu, ndi kupatuka m'njira ndikuuzani lero lino, kutsata milungu yina imene simunaidziwa.

Deuteronomo 11

Deuteronomo 11:21-32