Deuteronomo 11:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndidzapatsa mvula ya dziko lanu m'nyengo yace, ya myundo ndi ya masika, kuti mutute tirigu wanu, ndi vinyo wanu, ndi mafuta anu.

Deuteronomo 11

Deuteronomo 11:11-22