Deuteronomo 10:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Makolo anu anatsikira ku Aigupto ndiwo anthu makumi asanu ndi awiri; ndipo Yehova Mulungu wanu anakusandulizani tsopano mucuruke ngati nyenyezi za kumwamba.

Deuteronomo 10

Deuteronomo 10:15-22