Deuteronomo 10:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova anakondwera nao makolo anu kuwakonda, nasankha mbeu zao zakuwatsata, ndiwo inu, mwa mitundu yonse ya anthu, monga kuli lero lino.

Deuteronomo 10

Deuteronomo 10:11-20