Deuteronomo 1:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana anu amene mudanena, Adzakhala ogulidwa, ndi ana anu osadziwa cabwino kapena coipa ndi pano, iwo adzalowamo, ndidzawapatsa iwo ili, adzalilandira ndi iwo.

Deuteronomo 1

Deuteronomo 1:35-42