Danieli 9:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

inde pakunena ine m'kupemphera, munthu uja Gabrieli, amene ndidamuona m'masomphenya poyamba paja, anauluka mwaliwiro nandikhudza ngati nthawi yakupereka nsembe ya madzulo.

Danieli 9

Danieli 9:12-27