Danieli 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, Mulungu wathu, mumvere pemphero la mtumiki wanu, ndi mapembedzero ace, nimuwalitse nkhope yanu pa malo anu opatulika amene ali opasuka, cifukwa ca Ambuye,

Danieli 9

Danieli 9:12-19