Danieli 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

sitinamvera mau a Yehova Mulungu wathu, kuyenda m'malamulo ace anatiikirawo pamaso pathu, mwa atumiki ace aneneri.

Danieli 9

Danieli 9:7-17