Danieli 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadzera nkhosa yamphongoyo yokhala ndi nyanga ziwiri, imene ndidaiona irikuima kumtsinje, naithamangira ndi mphamvu yace yaukali.

Danieli 8

Danieli 8:1-7