Danieli 8:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ine Danieli ndinakomoka ndi kudwala masiku ena; pamenepo ndinauka ndi kucita nchito ya mfumu; ndipo ndinadabwa nao masomphenyawo, koma panalibe wakuwazindikiritsa.

Danieli 8

Danieli 8:22-27