Danieli 8:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona m'masomphenya; tsono kunali, pakuwaona ine ndinali m'Susani, m'nyumba ya mfumu, ndiwo m'dziko la Elamu; ndinaona m'masomphenya kuti ndinali kumtsinje Ulai.

Danieli 8

Danieli 8:1-3