Danieli 7:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, cirombo cina caciwiri cikunga cimbalangondo cinatundumuka mbali imodzi; ndi m'kamwa mwace munali nthiti zitatu pakati pa mano ace; ndipo anatero naco, Nyamuka, lusira nyama zambiri.

Danieli 7

Danieli 7:2-9