Danieli 7:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kutha kwace kwa cinthuci nkuno. Ine Danieli, maganizo anga anandibvuta kwambiri, ndi nkhope yanga inasandulika; koma ndinasunga cinthuci m'mtima mwanga.

Danieli 7

Danieli 7:21-28