Danieli 7:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinayandikira kwa wina wa iwo akuimako ndi kumfunsa za coonadi za ici conse. Ndipo ananena nane, nandidziwitsa kumasulira kwace kwa zinthuzi:

Danieli 7

Danieli 7:15-17