Danieli 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anayankha, nati pamaso pa mfumu, Danieli uja wa ana a ndende a Yuda sasamalira inu, mfumu, kapena coletsa munacitsimikizaco; koma apempha pemphero lace katatu tsiku limodzi.

Danieli 6

Danieli 6:8-22