Danieli 5:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Usiku womwewo Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa.

31. Ndipo Dariyo Mmedi analandira ufumuwo ali wa zaka makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri.

Danieli 5