Danieli 5:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Belisazara analamulira, ndipo anabveka Danieli cibakuwa, ndi unyolo wagolidi m'khosi mwace, nalalikira za iye kuti ndiye wolamulira wacitatu m'ufumumo.

Danieli 5

Danieli 5:28-31