Danieli 5:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pokwezeka mtima wace, nulimba mzimu wace kucita modzikuza, anamtsitsa pa mpando wa ufumu wace, namcotsera ulemerero wace;

Danieli 5

Danieli 5:14-29