Danieli 5:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mfumu inu, Mulungu Wam'mwambamwamba anapatsa Nebukadinezara atate wanu ufumuwu, ndi ukulu, ndi ulemerero, ndi cifumu;

Danieli 5

Danieli 5:8-22