Danieli 5:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsono anabwera nao kwa ine anzeru, openda, kuti awerenge lemba ilo, ndi kundidziwitsa kumasulira kwace; koma sanakhoza kufotokozera kumasulira kwa cinthuci.

Danieli 5

Danieli 5:6-16