Danieli 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo analowa naye Danieli kwa mfumu. Mfumu inayankha, niti kwa Danieli, Ndiwe kodi Danieli uja wa ana a ndende a Yuda, amene mfumu atate wanga anatenga ku Yuda?

Danieli 5

Danieli 5:3-17