Danieli 4:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi okhala pa dziko lapansi onse ayesedwa acabe; ndipo Iye acita mwa cifunito cace m'khamu la kumwamba ndi mwa okhala pa dziko lapansi; ndipo palibe woletsa dzanja lace, kapena wakunena naye, Mucitanji?

Danieli 4

Danieli 4:29-37