Danieli 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ha! zizindikilo zace nzazikuru, ndi zozizwa zace nza mphamvu, ufumu wace ndiwo ufumu wosatha, ndi kulamulira kwace ku mibadwo mibadwo.

Danieli 4

Danieli 4:1-7