Danieli 4:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mtima wace usandulike, usakhalenso mtima wa munthu, apatsidwe mtima wonga wa nyama, nizimpitire nthawi zisanu ndi ziwiri.

Danieli 4

Danieli 4:7-19