Danieli 4:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anapfuulitsa, natero, Likhani mtengowo, sadzani nthambi zace, yoyolani masamba ace, mwazani zipatso zace, nyama zicoke pansi pace, ndi mbalame pa nthambi zace.

Danieli 4

Danieli 4:11-23