Danieli 3:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti pakumva inu mau a lipenga, citoliro, zeze, sansi, cisakasa, ngoli, ndi zoyimbitsa ziri zonse, mugwadire ndi kulambira fano lagolidi adaliimika mfumu Nebukadinezara;

Danieli 3

Danieli 3:1-9