Danieli 3:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu Nebukadinezara anadabwa, nauka msanga, nanena nati kwa mandoda ace, Kodi sitinaponya amuna atatu omangidwa m'kati mwa moto? Anayankha nati kwa mfumu, Inde mfumu.

Danieli 3

Danieli 3:19-26