Danieli 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo amuna awa anamangidwa ali cibvalire zopfunda zao, maraya ao, ndi nduwira zao, ndi zobvala zao zina; naponyedwa m'kati mwa ng'anjo yotentha yamoto.

Danieli 3

Danieli 3:19-28