Danieli 2:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Danieli anapempha mfumu, ndipo anaika Sadrake, Mesake, ndi Abedinego, ayang'anire nchito za dera la ku Babulo. Koma Danieli anakhala m'bwalo la mfumu.

Danieli 2

Danieli 2:43-49