Danieli 2:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Umo mudaonera kuti mwala unasemedwa m'phiri popanda manja, ndi kuti udapera citsulo, mkuwa, dongo, siliva, ndi golidi; Mulungu wamkuru wadziwitsa mfumu cidzacitika m'tsogolomo; lotoli nloona, ndi kumasulira kwace kwakhazikika.

Danieli 2

Danieli 2:37-48