Danieli 2:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi umo mudaonera citsulo cosanganizika ndi dongo, iwo adzadzisokoneza ndi ana a anthu wamba; koma sadzapharikizana, monga umo citsulo sicimasanganizikana ndi dongo.

Danieli 2

Danieli 2:37-49