Danieli 2:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ufumu wacinai udzakhala wolimba ngati citsulo, popeza citsulo ciphwanya ndi kufoketsa zonse; ndipo monga citsulo ciswa zonsezi, uwu udzaphwanya ndi kuswa.

Danieli 2

Danieli 2:34-47