Danieli 2:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo pali ponse pokhala ana a anthu Iye anapereka nyama za kuthengo, ndi mbalame za m'mlengalenga, m'dzanja lanu; nakucititsani ufumu pa izi zonse; inu ndinu mutuwo wagolidi.

Danieli 2

Danieli 2:31-44