Danieli 2:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munali cipenyere kufikira mwala unasemedwa popanda manja, umene unagunda fanoli pa mapazi ace okhala citsulo ndi dongo, nuwaphwanya.

Danieli 2

Danieli 2:30-37